Ekisodo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Ndiyeno upange chihema chopatulika ndi nsalu 10 zopangira hema.+ Nsaluzo zikhale zaulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira+ ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo akerubi.+
26 “Ndiyeno upange chihema chopatulika ndi nsalu 10 zopangira hema.+ Nsaluzo zikhale zaulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira+ ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo akerubi.+