Deuteronomo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+
5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+