Yeremiya 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 mverani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo ndipo mwalowadi m’dzikolo ndi kukhala kumeneko monga alendo,+ Luka 9:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamene masiku oti akwere kumwamba+ anali kukwana, anatsimikiza mtima kupita ku Yerusalemu.
15 mverani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo ndipo mwalowadi m’dzikolo ndi kukhala kumeneko monga alendo,+