1 Mafumu 8:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.” 2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ Maliko 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+
61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.”
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+
30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+