2 Samueli 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi, Davide anabereka ana aamuna+ ku Heburoni,+ ndipo mwana wake woyamba anali Aminoni+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli. 1 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+
2 Pa nthawiyi, Davide anabereka ana aamuna+ ku Heburoni,+ ndipo mwana wake woyamba anali Aminoni+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli.
5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+