2 Samueli 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali+ m’dera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho+ kwa iye. Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene wapita.+ 1 Mbiri 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anamanga midzi ya asilikali m’dera la Asiriya a ku Damasiko,+ ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho kwa iye.+ Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali+ m’dera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho+ kwa iye. Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene wapita.+
6 Ndiyeno Davide anamanga midzi ya asilikali m’dera la Asiriya a ku Damasiko,+ ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho kwa iye.+ Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+