2 Samueli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide wochokera ku mitundu yonse imene inagonjetsa.+ Ezara 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndi kutinso munyamule siliva ndi golide zimene mfumu ndi aphungu ake apereka mwaufulu+ kwa Mulungu wa Isiraeli, amene amakhala ku Yerusalemu.+ Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+
11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide wochokera ku mitundu yonse imene inagonjetsa.+
15 ndi kutinso munyamule siliva ndi golide zimene mfumu ndi aphungu ake apereka mwaufulu+ kwa Mulungu wa Isiraeli, amene amakhala ku Yerusalemu.+