Genesis 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+ Deuteronomo 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Isiraeli analira Mose m’chipululu cha Mowabu masiku 30.+ Ndiyeno masiku onse olira maliro a Mose anatha.
10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+
8 Ana a Isiraeli analira Mose m’chipululu cha Mowabu masiku 30.+ Ndiyeno masiku onse olira maliro a Mose anatha.