2 Mbiri 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nkhani zina+ zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zosonyeza kukoma mtima kosatha,+ zinalembedwa m’masomphenya a mneneri Yesaya mwana wa Amozi,+ m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli. Miyambo 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+
32 Nkhani zina+ zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zosonyeza kukoma mtima kosatha,+ zinalembedwa m’masomphenya a mneneri Yesaya mwana wa Amozi,+ m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.
22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+