Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+ Yoswa 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo,+ monga mmene anakulonjezerani.+
30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+
10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo,+ monga mmene anakulonjezerani.+