Numeri 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mwana woyamba kubadwa aliyense pakati pa ana a Isiraeli ndi wanga, kaya akhale wa munthu kapena wa nyama.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana woyamba kubadwa aliyense m’dziko la Iguputo+ ndinawapatula kuti akhale anga.+
17 Mwana woyamba kubadwa aliyense pakati pa ana a Isiraeli ndi wanga, kaya akhale wa munthu kapena wa nyama.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana woyamba kubadwa aliyense m’dziko la Iguputo+ ndinawapatula kuti akhale anga.+