Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Levitiko 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Munthu asapatule nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yoyera, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ng’ombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+
2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
26 “‘Munthu asapatule nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yoyera, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ng’ombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+