Numeri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Mose anamva anthu akulira m’mabanja mwawo, munthu aliyense pakhomo la hema wake. Pamenepo mkwiyo wa Yehova unawayakira koopsa anthuwo.+ Mose nayenso anaipidwa nazo zimenezo.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.
10 Tsopano Mose anamva anthu akulira m’mabanja mwawo, munthu aliyense pakhomo la hema wake. Pamenepo mkwiyo wa Yehova unawayakira koopsa anthuwo.+ Mose nayenso anaipidwa nazo zimenezo.+
5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.