6 Aisiraeli anatenga ana aakazi a Akanani kukhala akazi awo,+ ndipo ana awo aakazi anawapereka kwa ana aamuna a Akanani,+ moti Aisiraeli anayamba kutumikira milungu ya Akanani.+
27 “Choncho iwe mwana wa munthu, lankhula ndi nyumba ya Isiraeli ndipo uwauze kuti,+ ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Makolo anu anandilankhulira mawu onyoza pamene anali kundichitira zinthu mosakhulupirika.+