Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+
13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+