Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Ezekieli 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+ Amosi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’ Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+
4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’
27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+