Ekisodo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ chonde ndidziwitseni njira zanu,+ kuti ndikudziweni, kutinso mundikomere mtima. Ndipo kumbukirani kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+ Salimo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+ Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+ Salimo 143:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+
13 Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ chonde ndidziwitseni njira zanu,+ kuti ndikudziweni, kutinso mundikomere mtima. Ndipo kumbukirani kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+
8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+
11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+
8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+