Salimo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+ Zekariya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+
19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+
17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+