Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+