Miyambo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wanga, mvetsera nzeru zanga.+ Tchera makutu ako ku zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kuzindikira,+ Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+ Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+ Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+
5 Mwana wanga, mvetsera nzeru zanga.+ Tchera makutu ako ku zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kuzindikira,+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+
5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+