Salimo 119:103 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Mawu anu amatsekemera m’kamwa mwanga,Kuposa mmene uchi umakomera!+ Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+ Miyambo 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 M’njira yomweyo, dziwa nzeru kuti upindule.+ Ukazipeza, udzakhala ndi tsogolo labwino ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+
14 M’njira yomweyo, dziwa nzeru kuti upindule.+ Ukazipeza, udzakhala ndi tsogolo labwino ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+