Genesis 43:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndikhala chikole cha moyo wa mnyamatayu.+ Chilangocho chikabwere pa ine.+ Ndikadzalephera kubwera naye ndi kum’pereka kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu moyo wanga wonse. Miyambo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+ Miyambo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+
9 Ineyo ndikhala chikole cha moyo wa mnyamatayu.+ Chilangocho chikabwere pa ine.+ Ndikadzalephera kubwera naye ndi kum’pereka kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu moyo wanga wonse.
18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+
26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+