Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+ Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Numeri 35:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+ Deuteronomo 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti akanthe ndi kupheratu munthu, kuti akhetse magazi a munthu wosachimwa.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+
25 “‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti akanthe ndi kupheratu munthu, kuti akhetse magazi a munthu wosachimwa.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)