6 “Undiike pamtima pako ngati chidindo,+ ndiponso undiike ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi n’champhamvu ngati imfa.+ Mofanana ndi Manda, chikondi sichigonja ndipo chimafuna kudzipereka ndi mtima wonse.+ Kuyaka kwake kuli ngati kuyaka kwa moto. Chikondicho ndi lawi la Ya.+