2 Mafumu 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+ Salimo 112:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ Miyambo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndi bwino kusankha dzina labwino kusiyana ndi chuma chochuluka.+ Kulemekezedwa kuli bwino kuposa siliva ndi golide.+ Mlaliki 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mbiri yabwino imaposa mafuta onunkhira,+ ndipo tsiku lomwalira limaposa tsiku lobadwa.+
34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+
6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+
22 Ndi bwino kusankha dzina labwino kusiyana ndi chuma chochuluka.+ Kulemekezedwa kuli bwino kuposa siliva ndi golide.+