Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 72:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!* Yesaya 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.
19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!*
15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.