-
Yesaya 57:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Pakuti Wapamwamba ndi Wokwezeka,+ yemwe adzakhalepo kwamuyaya+ ndiponso yemwe dzina lake ndi loyera,+ wanena kuti: “Ine ndimakhala kumwamba pamalo oyera.+ Ndimakhalanso ndi munthu wopsinjika ndi wa mtima wodzichepetsa,+ kuti nditsitsimutse mtima wa anthu onyozeka ndiponso kuti nditsitsimutse mtima wa anthu opsinjika.+
-
-
Aroma 16:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Koma tsopano chinsinsi chopatulika chimenechi chaonetsedwa+ ndipo chadziwika pakati pa mitundu yonse ya anthu kudzera m’malemba aulosi. Zimenezi n’zogwirizana ndi lamulo la Mulungu wokhalako kwamuyaya. Cholinga chake n’chakuti anthu a mitundu yonse amukhulupirire ndi kumumvera mwa chikhulupiriro.+
-