Yesaya 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mitundu yonse ndi yopanda pake pamaso pake.+ Amaiona ngati si kanthu n’komwe, ngati kuti iyo kulibe.+ Yesaya 60:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti mtundu uliwonse ndi ufumu uliwonse umene sudzakutumikira udzawonongedwa, ndipo mitundu ya anthu idzasakazidwa ndithu.+
17 Mitundu yonse ndi yopanda pake pamaso pake.+ Amaiona ngati si kanthu n’komwe, ngati kuti iyo kulibe.+
12 Pakuti mtundu uliwonse ndi ufumu uliwonse umene sudzakutumikira udzawonongedwa, ndipo mitundu ya anthu idzasakazidwa ndithu.+