Yesaya 41:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nenani zinthu zimene zikubwera m’tsogolo, kuti tidziwe kuti inu ndinu milungu.+ Inde, muyenera kuchita zabwino kapena zoipa, kuti tizionere limodzi ndi kuchita mantha.+ Yesaya 43:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Ndikupanga zinthu zatsopano.+ Zimenezi zionekera ndipo anthu inu muzidziwa ndithu.+ M’chipululu, ine ndidzatsegulamo njira+ ndi mitsinje.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+ 2 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+
23 Nenani zinthu zimene zikubwera m’tsogolo, kuti tidziwe kuti inu ndinu milungu.+ Inde, muyenera kuchita zabwino kapena zoipa, kuti tizionere limodzi ndi kuchita mantha.+
19 Taonani! Ndikupanga zinthu zatsopano.+ Zimenezi zionekera ndipo anthu inu muzidziwa ndithu.+ M’chipululu, ine ndidzatsegulamo njira+ ndi mitsinje.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+