Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+