Yesaya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+ Yeremiya 51:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.
20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+
39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.