Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+ Yeremiya 52:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumu ya Babulo inapha anthu amenewa+ ku Ribila+ m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+
27 Mfumu ya Babulo inapha anthu amenewa+ ku Ribila+ m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+