Ezekieli 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali a kumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala khamu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu chankhondo. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+ Ezekieli 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Ndidzatumiza moto ku Magogi+ ndi kwa anthu amene akukhala mwabata m’zilumba,+ ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali a kumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala khamu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu chankhondo. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+
6 “‘Ndidzatumiza moto ku Magogi+ ndi kwa anthu amene akukhala mwabata m’zilumba,+ ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.