Ekisodo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+ Yesaya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Wagwa kuchokera kumwamba,+ wonyezimirawe, iwe mwana wa m’bandakucha! Wadulidwa n’kugwera padziko lapansi,+ iwe amene unali kupundula mitundu.+ Yeremiya 50:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taona! Iwe Babulo Wodzikuza,+ ndikukuthira nkhondo,”+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ “Pakuti tsiku lako lifika, nthawi imene ndiyenera kukulanga. Ezekieli 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘“Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako wonyezimira.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi+ ndipo mafumu azidzakuyang’ana.+
16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+
12 “Wagwa kuchokera kumwamba,+ wonyezimirawe, iwe mwana wa m’bandakucha! Wadulidwa n’kugwera padziko lapansi,+ iwe amene unali kupundula mitundu.+
31 “Taona! Iwe Babulo Wodzikuza,+ ndikukuthira nkhondo,”+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ “Pakuti tsiku lako lifika, nthawi imene ndiyenera kukulanga.
17 “‘“Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako wonyezimira.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi+ ndipo mafumu azidzakuyang’ana.+