Genesis 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo. Danieli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinalota maloto amene anayamba kundichititsa mantha.+ Ndili pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya m’maganizo mwanga. Zimenezi zinayamba kundichititsa mantha.+
8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo.
5 Kenako ndinalota maloto amene anayamba kundichititsa mantha.+ Ndili pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya m’maganizo mwanga. Zimenezi zinayamba kundichititsa mantha.+