Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+