Yobu 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+
15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+