-
Zekariya 5:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno anandiuza kuti: “Ili ndi temberero limene likubwera padziko lonse lapansi,+ chifukwa aliyense amene akuba+ sakulandira chilango, monga mmene temberero limene lalembedwa kumbali imodzi ya mpukutuwo likunenera. Komanso aliyense amene akulumbira mwachinyengo+ sakulandira chilango, monga mmene temberero limene lalembedwa kumbali inayo ya mpukutuwo likunenera.+
-