Ekisodo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Polowa m’chihema chokumanako, kapena popita kukatumikira paguwa lansembe, kukapereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto,+ azisamba kuti asafe. 1 Akorinto 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi simukudziwa kuti anthu ochita ntchito zopatulika amadya+ za m’kachisi, ndipo amene amatumikira+ kuguwa lansembe nthawi zonse amagawana gawo ndi guwa lansembe?
20 Polowa m’chihema chokumanako, kapena popita kukatumikira paguwa lansembe, kukapereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto,+ azisamba kuti asafe.
13 Kodi simukudziwa kuti anthu ochita ntchito zopatulika amadya+ za m’kachisi, ndipo amene amatumikira+ kuguwa lansembe nthawi zonse amagawana gawo ndi guwa lansembe?