Chivumbulutso 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi yomweyo, ndinamuyankha kuti: “Mbuyanga, mukudziwa ndinu.” Ndipo iye anati: “Amenewa ndi amene atuluka m’chisautso chachikulu,+ ndipo achapa mikanjo yawo ndi kuiyeretsa+ m’magazi+ a Mwanawankhosa.
14 Nthawi yomweyo, ndinamuyankha kuti: “Mbuyanga, mukudziwa ndinu.” Ndipo iye anati: “Amenewa ndi amene atuluka m’chisautso chachikulu,+ ndipo achapa mikanjo yawo ndi kuiyeretsa+ m’magazi+ a Mwanawankhosa.