Yakobo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamang’ung’udzirane abale, kuopera kuti mungaweruzidwe.+ Taonani, Woweruza waima pakhomo.+