Luka 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+
42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+