Mateyu 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Lekani kudera nkhawa+ moyo wanu kuti mudzadya chiyani, kapena mudzamwa chiyani, kapenanso kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo suposa chakudya, ndipo kodi thupi siliposa chovala?+ 1 Timoteyo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, pokhala ndi chakudya, zovala ndi pogona, tikhale okhutira ndi zinthu zimenezi.+
25 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Lekani kudera nkhawa+ moyo wanu kuti mudzadya chiyani, kapena mudzamwa chiyani, kapenanso kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo suposa chakudya, ndipo kodi thupi siliposa chovala?+