Salimo 118:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana+Wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.+ Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’? 1 Petulo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa ndinu okhulupirira, koma kwa osakhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri,”+
16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+
42 Ndiyeno Yesu anawafunsa kuti: “Kodi simunawerenge zimene Malemba amanena zakuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana+ ndi umene wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.+ Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?
7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa ndinu okhulupirira, koma kwa osakhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ umenewu wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri,”+