Luka 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+ Machitidwe 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo woyang’anira kachisi uja ananyamuka ndi alonda ake n’kukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa+ kuti anthu awaponya miyala.
2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+
26 Pamenepo woyang’anira kachisi uja ananyamuka ndi alonda ake n’kukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa+ kuti anthu awaponya miyala.