Deuteronomo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifaniziro cha nyama iliyonse ya padziko lapansi,+ chifaniziro cha mbalame iliyonse youluka m’mlengalenga,+ Ezekieli 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.
17 chifaniziro cha nyama iliyonse ya padziko lapansi,+ chifaniziro cha mbalame iliyonse youluka m’mlengalenga,+
10 Chotero ine ndinalowa, ndipo ndinaona kuti pamakoma anajambulapo zithunzi+ za nyama iliyonse yokwawa, za chilombo chilichonse chonyansa+ ndi za mafano onse onyansa a nyumba ya Isiraeli.+ Pamakoma onse anajambulapo zithunzizo mochita kugoba.