Machitidwe 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+ Aroma 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abale amene ali ku Makedoniya ndi ku Akaya+ akhala ali ofunitsitsa kupereka+ mphatso kwa oyera osauka a ku Yerusalemu.
17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+
26 Abale amene ali ku Makedoniya ndi ku Akaya+ akhala ali ofunitsitsa kupereka+ mphatso kwa oyera osauka a ku Yerusalemu.