Aroma 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Si zokhazo ayi, komanso ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira+ zomwe ndi mzimu, tikubuula+ mumtima mwathu pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti titengedwe kukhala ana a Mulungu,+ kumasulidwa ndi dipo* kuti tituluke m’matupi athu.
23 Si zokhazo ayi, komanso ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira+ zomwe ndi mzimu, tikubuula+ mumtima mwathu pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti titengedwe kukhala ana a Mulungu,+ kumasulidwa ndi dipo* kuti tituluke m’matupi athu.