1 Yohane 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa mādziko.+
4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa mādziko.+