Aroma 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwaubale.+ Mipingo yonse ya Khristu ikupereka moni. 1 Akorinto 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale onse akukupatsani moni. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.+ 2 Akorinto 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwaubale.+